Look for any podcast host, guest or anyone
Showing episodes and shows of

John Joseph Matandika

Shows

Chuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiUmunthu wa Yesu KhristuPACHIYAMBI panali Mawu, ndipo Mawu adali ndi Mulungu, ndipo Mawu adali Mulungu. Awa adali pachiyambi ndi Mulungu. Zinthu zonse zidalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikadalengedwa kanthu kena kali konse kolengedwa. Mwa Iye mudali moyo; ndi moyowu udali kuwunika kwa anthu. Ndipo kuwunikaku kudawala mumdima; ndi mdimawu sudakuzindikira. Kudali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane. Iyeyu adadza mwa umboni, kudzachita umboni za kuwunikaku, kuti anthu onse kudzera mwa iye akakhulupirire. Iye sindiye kuwunikaku, koma adatumidwa kukachita umboni wa kuwunikaku. Uku ndiko kuwunika kwenikweni kumene kuwunikira anthu onse akulowa m’dziko lapansi. Adali m’dziko lapansi, ndipo dziko lapa...2022-05-2428 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 6Usaphe.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2425 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 10Usasirire.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 8Usabe.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 7Usachite chigololo.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado m...2022-05-2422 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 9Usapereke umboni omunamizila mzako.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi ch...2022-05-2424 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNsembe Yokwanilitsa Chilungamo cha MulunguKuzunzika ndi Ulemerero wa Mtumiki13Taonani, mtumiki wanga adzapambana pa ntchito yakeadzakwezedwa ndi kulemekezedwa ndipo adzalandira ulemu waukulu kwambiri.14Anthu ambiri atamuona anadzidzimuka,chifukwa nkhope yake inali itasakazika; sinalinso ngati ya munthu.Ndipo thupi lake linasakazika; silinalinso ngati la munthu.15Momwemonso anthu a mitundu yonse adzadodoma naye,ndipo mafumu adzatseka pakamwa pawo kusowa chonena chifukwa cha iye.Pakuti zinthu zimene iwo sanawuzidwepo, adzaziona,ndipo zimene sanazimvepo, adzazimvetsa.2022-05-2424 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKugwa kwa MunthuKuchimwa kwa Munthu1Ndipo njoka inali yochenjera kuposa nyama yakuthengo iliyonse imene Yehova Mulungu anapanga. Njokayo inati kwa mkaziyo, “Kodi Mulungu ananenadi kuti, ‘Inu musadye zipatso za mtengo uliwonse mʼmundamu?’ ”2Mkaziyo anati kwa njokayo, “Tikhoza kudya zipatso za mʼmitengo ya mʼmundawu, 3koma Mulungu anati, ‘Musadye zipatso za mu mtengo umene uli pakati pa munda, ndipo musadzawukhudze kuti mungadzafe.’ ”4“Ndithudi simudzafa,” inatero njokayo kwa mkaziyo. 5“Pakuti Mulungu akudziwa kuti tsiku limene mudzadye zipatso za mu mtengowo, maso anu adzatsekuka, ndipo mudzakhala ngati Mulungu, wodziwa zabwino ndi zoyipa.”6Pamene mkaziyo anaona kuti mtengowo unali wabw...2022-05-2427 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKulemekeza kwa Anzeru a ku M'mawaNdipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m’masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum’mawa anafika ku Yerusalemu, Nanena, Ali kuti amene adabadwa mfumu ya Ayuda? Chifukwa tidawona nyenyezi yake kum’mawa, ndipo tidabwera kudzamlambira Iye. Pamene Herode mfumuyo adamva ichi adavutika, ndi Yerusalemu yense pamodzi naye. Ndipo pamene adasonkhanitsa ansembe akulu onse ndi alembi a anthu, adafunsira iwo, adzabadwira kuti Khristuyo? Ndipo adamuwuza iye, M’Betelehemu wa Yudeya; chifukwa kudalembedwa kotere ndi m’neneri kuti, Ndipo iwe Betelehemu, dziko la Yudeya, sukhala konse wam’ng’onong’ono mwa akulu a Yudeya; pakuti wotsogolera adzachokera mwa...2022-05-2427 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKufunikila kwa Imfa ya Ambuye YesuKoma atafika Khristu, Mkulu wansembe wa zabwino ziri mkudza, mwa chihema chachikulu ndi changwiro choposa, chosamangika ndi manja, ndiko kunena kuti, chosati cha chilengedwe ichi; Kosati mwa mwazi wa mbuzi ndi ana ang’ombe, koma mwa mwazi wa Iye yekha, adalowa kamodzi kumalo wopatulika, atalandirapo chiwombolo chosatha chifukwa cha ife. Pakuti ngati mwazi wa mbuzi ndi ng’ombe zamphongo, ndi makala ang’ombe yamthandi wowazawaza pa iwo wodetsedwa, upatutsa kufikira chiyeretso cha thupi: Koposa kotani nanga mwazi wa Khristu amene adadzipereka yekha wopanda chilema kwa Mulungu mwa Mzimu wosatha, udzayeretsa chikumbumtima chanu kuchisiyanitsa ndi ntchito zakufa, kukatumikira Mulungu wamoyo? Ndipo...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMtanda OdabwitsaNdipo pomwepo m`mawa adakhala upo ansembe akulu, ndi akulu a anthu, ndi alembi, ndi akulu a milandu onse, namanga Yesu, namtenga, nampereka kwa Pilato. Ndipo Pilato adamfunsa Iye, Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda? Ndipo poyankha adati kwa iye, Mwatero ndinu. Ndipo ansembe akulu adamnenera Iye zinthu zambiri koma sadayakhe kanthu. Ndipo Pilato adamfunsanso, nanena, Suyankha kanthu kodi? Tawona, akuchitira umboni Iwe mokutsutsa zinthu zambiri zotere. Koma Yesu sadayankhenso kanthu; kotero Pilato adazizwa. Tsopano amkawamasulira paphwando wa mndende m’modzi, amene iwo adamfuna. Ndipo adalipo wina dzina lake Baraba, womangidwa pamodzi ndi ena wopanduka, amene adapha munthu mumpanduko. Ndipo kh...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKubadwa mwa Namwali KodabwitsaTsoka kwa inu, pamene anthu adzanenera inu zabwino! Pakuti makolo awo adawatero momwemo aneneri wonama. Koma ndinena kwa inu akumva, kondanani nawo adani anu; chitirani zabwino iwo akuda inu. Dalitsani iwo akutemberera inu, pemphererani iwo akuchitira inu chipongwe. Ndipo kwa Iye amene akupanda iwe pa tsaya limodzi umpatsenso limzake; ndi iye amene alanda chofunda chako, usamkanize malaya akonso. Munthu aliyense akakupempha kanthu, umpatse; ndi iye amene alanda zako, usazipemphanso. Ndipo monga mufuna inu kuti anthu adzakuchitireni inu, muwachitire iwo motero inu momwemo. Ndipo ngati muwakonda iwo akukondana ndinu, mudzalandira chiyamiko chotani? Pakuti wochimwa womwe akonda iwo akukondana nawo. Ndipo...2022-05-2430 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiZochitika pa Kubadwa kwa YesuAmbuye wathu Yesu Khristu anabadwa modabwitsa. Luka 2:1-7Ndipo kudali masiku aja, kuti lamulo lidatuluka kwa Kayisala Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe. Ndiko kulembera koyamba pokhala Kureniyo kazembe wa Suriya. Ndipo onse adapita kukalembedwa, munthu aliyense ku mzinda wake. Ndipo Yosefe yemwe adakwera kuchokera ku Galileya, ku mzinda wa Nazarete, kupita ku Yudeya, ku mzinda wa Davide, dzina lake Betelehemu, (chifukwa iye adali wa banja ndi fuko lake la Davide:) Kukalembedwa iye mwini pamodzi ndi Mariya, wopalidwa naye ubwenzi; ndi uyu adali ndi pakati. Ndipo panali pokhala iwo komweko, masiku ake a kubala adakwanira kuti...2022-05-2429 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo LachisanuMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0824 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo LachinayiMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0825 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMalamulo Khumi Gawo 2Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0825 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMalamulo Khumi Gawo 1Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0827 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiUdindo wa MunthuMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0824 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKubadwa kwa YohaneAneneratu za Kubadwa kwa Yohane Mʼbatizi5Mʼmasiku a Herode, mfumu ya Yudeya, kunali wansembe dzina lake Zakariya wa gulu la ansembe la Abiya; mkazi wake Elizabeti analinso wa fuko la Aaroni. 6Onse awiri anali olungama pamaso pa Mulungu, ndipo amasunga malamulo ndi malangizo onse a Ambuye osalakwa konse. 7Koma analibe ana chifukwa Elizabeti anali wosabereka; ndipo onse anali okalamba.8Nthawi yogwira ntchito yotumikira ansembe a gulu la Zekariya, Zekariya ankatumikira ngati wansembe pamaso pa Mulungu, 9Zakariyayo anasankhidwa mwa maere, monga mwa mwambo wa unsembe, kupita mʼNyumba ya Ambuye kukafukiza lubani. 10Ndipo nthawi yof...2022-03-0828 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKubadwa kwa YesuMakolo a Yesu Khristu Monga mwa Thupi1Buku lofotokoza za mʼbado wa Yesu Khristu mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu:2Abrahamu anabereka Isake,Isake anabereka Yakobo,Yakobo anabereka Yuda ndi abale ake.3Yuda anabereka Perezi ndi Zara, amene amayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi,Hezironi anabereka Aramu.4Aramu anabereka Aminadabu,Aminadabu anabereka Naasoni,Naasoni anabereka Salimoni.5Salimoni anabereka Bowazi amene amayi ake anali Rahabe,Bowazi anabereka Obedi amene amayi ake anali Rute,2022-03-0831 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTanthauzo la Pemphero Gawo LomalizaSalimo 1001Fuwulani kwa Yehova mwachimwemwe, inu dziko lonse lapansi.2Mulambireni Yehova mosangalala;bwerani pamaso pake ndi nyimbo zachikondwerero.3Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.Iye ndiye amene anatipanga ndipo ife ndife ake;ndife anthu ake, nkhosa za pabusa pake.4Lowani ku zipata zake ndi chiyamikondi ku mabwalo ake ndi matamando;muyamikeni ndi kutamanda dzina lake.5Pakuti Yehova ndi wabwino ndipo chikondi chake ndi chamuyaya;kukhulupirika kwake nʼkokhazikika pa mibado ndi mibado.2021-11-2126 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKusala ndi KulapaEksodo 34:28Mose anakhala kumeneko pamodzi ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku, wosadya kanthu kapena kumwa madzi. Ndipo iye analemba pa miyala ija mawu a pangano, malamulo khumi.Machitidwe 27:9Tinataya nthawi yayitali, ndipo kuyenda pa nyanja kunali koopsa chifukwa nʼkuti tsopano nthawi yosala kudya itapita kale. Choncho Paulo anawachenjeza kuti,2021-11-2125 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMapemphero EnaMateyu 26:36-4636Kenaka Yesu anapita ku malo otchedwa Getsemani, ndipo anawawuza kuti, “Khalani pano pamene Ine ndikukapemphera apo.” 37Anatenga Petro ndi ana awiri a Zebedayo, ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika mu mtima. 38Pamenepo anawawuza kuti, “Moyo wanga uli ndi chisoni chofa nacho. Khalani pano ndipo dikirani pamodzi ndi Ine.”39Atapita patsogolo pangʼono, anagwa pansi chafufumimba napemphera kuti, “Atate anga, ngati ndikotheka, chikho ichi chichotsedwe kwa Ine. Koma osati monga mmene ndifunira, koma monga mufunira Inu.”40Kenaka anabwera kwa ophunzira ake nawapeza ali mtulo. Iye anafunsa Petro kuti, “Kodi anthu inu, simukanakhala maso pamodzi nd...2021-11-2130 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiPemphero la Ambuye Gawo 29 “Chifukwa chake pempherani motere:“ ‘Atate athu akumwamba,dzina lanu lilemekezedwe,10 Ufumu wanu ubwere,chifuniro chanu chichitikepansi pano monga kumwamba.11 Mutipatse chakudya chathu chalero.12 Mutikhululukire mangawa athu,monga ifenso tawakhululukira amangawa athu.13 Ndipo musatitengere kokatiyesa;koma mutipulumutse kwa woyipayo.’2021-11-2124 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiPemphero la AmbuyeMateyu 6:9-139 “Chifukwa chake pempherani motere:“ ‘Atate athu akumwamba,dzina lanu lilemekezedwe,10 Ufumu wanu ubwere,chifuniro chanu chichitikepansi pano monga kumwamba.11 Mutipatse chakudya chathu chalero.12 Mutikhululukire mangawa athu,monga ifenso tawakhululukira amangawa athu.13 Ndipo musatitengere kokatiyesa;koma mutipulumutse kwa woyipayo.’2021-10-2727 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTipemphere Nthawi Yanji? Gawo 2Salimo 145:1-31Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu yanga;ndidzatamanda dzina lanu ku nthawi za nthawi.2Ndidzakutamandani tsiku ndi tsikundi kulemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi.3Yehova ndi wamkulu ndi woyenera matamando onse;ukulu wake palibe angawumvetsetse.2021-10-2729 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTipemphere Nthawi Yanji?Machitidwe 2:42-4742Iwo ankasonkhana pamodzi kuphunzitsidwa ndi atumwi, pachiyanjano, pachakudya ndi popemphera. 43Aliyense ankachita mantha chifukwa cha zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri zimene atumwi ankachita. 44Okhulupirira onse anali pamodzi ndipo aliyense ankapereka zinthu zake kuti zikhale za onse. 45Ankagulitsa minda yawo ndi katundu wawo, ndi kugawira kwa aliyense molingana ndi zosowa zake. 46Tsiku ndi tsiku ankasonkhana pamodzi pa bwalo la pa Nyumba ya Mulungu. Ankadya pamodzi mʼnyumba zawo mwasangala ndi mtima woona. 47Ankayamika Mulungu ndipo anthu onse ankawakomera mtima. Ndipo tsiku ndi tsiku Ambuye ankawonjezera ena pa chiwerengero cha olandira chipulumutso.2021-10-2727 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTipemphere Chifukwa Chiyani?LUKA 11Yesu Aphunzitsa za ku Pemphera1Tsiku lina Yesu amapemphera pamalo ena. Atamaliza, mmodzi wa ophunzira ake anati kwa Iye, “Ambuye tiphunzitseni kupemphera, monga momwe Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”2Yesu anawawuza kuti, “Pamene mukupemphera muzinena kuti:“ ‘Atate,dzina lanu lilemekezedwe,ufumu wanu ubwere.3 Mutipatse chakudya chathu chalero,4 mutikhululukire machimo athu,monga ifenso timakhululukira aliyense amene watilakwira.Ndipo musalole kuti tigwe mʼmayesero.’ ”2021-10-0731 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMagawo a Pemphero Gawo 2MASALIMO 3Salimo la Davide. Atathawa mwana wake Abisalomu.1Inu Yehova, achulukadi adani anga!Achulukadi amene andiwukira!2Ambiri akunena za ine kuti,“Mulungu sadzamupulumutsa.”Sela3Koma Inu Yehova, ndinu chishango chonditeteza,Inu mwandiveka ulemerero ndipo mwanditukula.4Kwa Yehova, Ine ndilira mofuwulandipo Iye amandiyankha kuchokera ku phiri lake loyera.Sela5Ine ndimagona ndi kupeza tulo;ndimadzukanso chifukwa Yehova amandichirikiza.6Sindidzaopa adani anga osawerengeka ameneabwera kulimbana nane kuchokera ku madera onse...2021-10-0725 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMagawo a PempheroMASALIMO 1361Yamikani Yehova chifukwa ndi wabwino.Pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.2Yamikani Mulungu wa milungu.Pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.3Yamikani Ambuye wa ambuye,pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.4Iye yekhayo amene amachita zodabwitsa zazikulu,pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.5Amene mwachidziwitso chake anapanga mayiko akumwamba,pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.6Amene anayala dziko lapansi pamwamba pa madzi,pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.7Amene anapanga miyuni ikuluikulu,p...2021-09-2124 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTanthauzo la PempheroAroma 8:26-2826Momwemonso, Mzimu amatithandiza ife mʼkufowoka kwathu. Ife sitidziwa momwe tiyenera kupempherera koma Mzimu mwini amatipempherera mobuwula ndi mawu osafotokozedwa. 27Koma Iye amene amasanthula mitima yathu amadziwa maganizo a Mzimu, chifukwa Mzimu amapempherera oyera mtima molingana ndi chifuniro cha Mulungu. 28Ndipo ife tikudziwa kuti zinthu zonse zimathandizana kuwachitira ubwino amene amakonda Mulungu, amene anayitanidwa monga mwa cholinga chake.2021-09-1827 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi tipemphere motani?Mateyu 6:5-85 “Pamene mupemphera, musakhale ngati achiphamaso, chifukwa iwo amakonda kupemphera choyimirira mʼmasunagoge ndi pa mphambano za mʼmisewu kuti anthu awaone. Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti iwo alandiriratu mphotho yawo yonse. 6Koma pamene mupemphera, lowani mʼchipinda chanu chamʼkati, ndi kutseka chitseko ndipo mupemphere kwa Atate anu amene saoneka. Ndipo Atate anu, amene amaona zochitika mseri, adzakupatsani mphotho. 7Ndipo pamene mukupemphera, musamabwerezabwereza monga akunja, pakuti iwo amaganiza kuti adzamveka chifukwa chochulutsa mawu. 8Musakhale ngati iwo chifukwa Atate anu amadziwa zimene musowa musanapemphe.2021-09-0429 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKukondana Wina ndi MnzakeMateyu 25:34-4034 “Pamenepo mfumu idzati kwa a ku dzanja lamanja, ‘Bwerani inu odalitsika ndi Atate anga; landirani ufumu umene unakonzedwa chifukwa cha inu kuyambira pachiyambi cha dziko. 35Pakuti ndinali ndi njala ndipo munandipatsa chakudya, ndinali ndi ludzu ndipo munandipatsa madzi akumwa, ndinali mlendo ndipo munandilandira, 36ndinali wausiwa ndipo munandiveka, ndinali wodwala ndipo munandisamalira, ndinali ku ndende ndipo inu munandiyendera.’37 “Ndipo olungamawo adzamuyankha kuti, ‘Ambuye ndi liti tinakuonani muli ndi njala ndipo tinakudyetsani, kapena ludzu ndipo tinakupatsani madzi akumwa? 38Ndi liti tinakuonani muli mlendo ndipo tinakulandirani, kapena wa usiwa ndipo tinakuvekani? 39Ndi liti tinakuonan...2021-09-0429 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKubwezana TikaloweleraPatokha timaloweleraGalatians 6:1Abale, ngati munthu agwa mʼtchimo lililonse, inu amene Mzimu amakutsogolerani, mumuthandize munthuyo ndi mtima wofatsa kuti akonzekenso. Koma mukhale maso kuti inu nomwe mungayesedwe.Yakobo 15:19-2019Abale anga, ngati mmodzi wa inu apatuka pa choonadi ndipo wina wake ndi kumubweza, 20kumbukirani izi: Aliyense wobweza wochimwa kuchoka ku cholakwa chake, adzamupulumutsa ku imfa ndi kukwirira machimo ambiri.Mpingo UmatibwezaMateyu 18:15-1715 “Ngati mʼbale wako akuchimwira, pita kamuwuze cholakwa chake pa awiri. Ngati akumvera, wamubweza mʼbale wakoyo. 16Koma ngati sakumvera, katenge wina...2021-08-1829 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKuphuzila kukonda Akhristu azathuLero tikupitiliza kulingalira zifukwa zimene tikusowekela kukhala pa mpingo.Sabata yatha, tidayamba kuyankha funso limeneli pakunena kuti tikusowekela mpingo popeza kuti timayanjanitsidwa ndi okhulupilira ena mwa Khristu komanso popeza timakula pamodzi kufikila kukula mwa Khristu ndi okhulupilira ena. Tikapanda kulabadila mpingo, zili ngati mamuna kusalabadila mkazi wake kapena gawo limodzi la thupi lanu kumakula mosagwilizana ndi thupi lonse. Zotsatila zake zitha kukhala zoyipa kuchitika zinthu zotele.Lero, tionjezela fundo ina pa yankho lathu, pamene tikufuna kuona kuti tikusowekela mpingo chifukwa cha kuti tikuyenela kuphuzila kukonda iwo amene Yesu amawakonda.Chimapangitsa ndi chiyani kuti...2021-08-1031 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKuyanjanitsidwa ndi KhristuLero tikufuna tione za kuyanjanitsidwa ndi Khristu komanso kukula pamodzi.Funso limene tingayambe nalo ndi lakuti; ndi chifukwa chiyani tikusowekela mpingo m’moyo mwathu? Masabata akubwela kutsogolowa tikhala tikuona kuti pali zifukwa zingapo zimene tikusowekela mpingo m’moyo mwathu. Sabata ino, tikhazikika pa zinthu ziwiri pamene tikuyankha funso limeneli. Timasowekela mpingo popeza tayanjanitsidwa ndi Khristu komanso chifukwa choti timakula pamodzi ndi anzathu osati patokha.Tikaona nkhani ya kuyanjanitsidwa ndi KhristuTiwelenge poyambaAroma 12:4-5“4Pakuti monga aliyense wa ife ali ndi thupi limodzi koma ziwalo zambiri, ziwalozi sizili ndi ntchit...2021-08-0329 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKukhala Membala Pa MpingoLero tikufuna tione za kukhala membala pa mpingoChiyambileni kuona za mpingo takhala tikuona za tanthauzo la mpingo komanso m’mene umagwilira ntchito. Koma zimatheka kuti anthu ambiri atha kumapemphela ndi anzawo pa mpingo koma sadutsa njira zimene zimafunikila kuti akhale membala wodziwika pa mpingo.Zimenezi zikuchulukila kwambiri mu chikhalidwe chathu lero lino. Anthu amene amadzitcha kuti ndi akhristu amatha kuchoka mpingo uwu kupita mpingo wina, kufunafuna zambiri kuti mwina akhale ndi moyo wauzimu opanda vuto. Ena atha kumapita ku tchalitchi koma safuna kukhala membala, bola azingopemphera nawo.Chimene tikuyenela kuzindikila ndi chakuti, si...2021-08-0329 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiChikhalidwe Komanso Tanthauzo la UbatizoTipite ku nkhani ya lero: chikhalidwe komanso tanthauzo la ubatizo.Tikuyenela tizindikile kuti nkhani ya ubatizo ndi nkhani imene yabweletsa mpungwepungwe pakati pa mipingo. Ndipo pena zimakhala zovetsa chisoni kuti akhristu amapezeka kuti akugawanikana pa nkhani imeneyi. Kusiyana kwathu pa nkhani ya ubatizo kusatisokoneze mu njira ina iliyonse. Chofunikila ndi kuonetsetsa kuti pa ziphuzitso zikuluzikulu za Baibulo komanso uthenga wabwino ndife ogwilizana. Nkhani ya tanthauzo komanso kachitidwe ka ubatizo kasakhale patsogolo ngati nkhani ya chipulumutso. Ikhale nkhani yobwela pambuyo.Pokhapokhapo pamene gulu lina la anthu litenga ubatizo ngati chipulumutso, tikuyenela kukanitsitsa ndi cholinga choti chipulumutso...2021-08-0330 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiChikhalidwe Komanso Tanthauzo la MgoneroChikhalidwe komanso Tanthauzo la Mgonero wa AmbuyeTikumbukile nthawi imene timakamba za masakalamenti pamene tidanena kuti alipo awiri: ubatizo komanso mgonero wa Ambuye.Masakalamenti amenewa adakhazikitsidwa ndi cholinga choti aonetsele poyera chikhulupiliro chathu cha uthenga wabwino. Pamene tikondwelera mu mgonero wa Ambuye komanso kutenga mbali pa ubatizo, zonsezi zimatipatsa mwayi oti tionetsele chikhulupiliro chathu poyera.Anthu atatipeza natifusa kuti kodi ndi chifukwa chiyani mukuchita izi. Yankho lake ndi lakuti, chifukwa cha chimene Yesu Khristu ali komanso zimene adachita. St. Augustine pokamba za masakalamenti adanena kuti: “zizindikilo zakunja komanso zooneka ndi maso za chisomo ch...2021-07-0927 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Tipembedze Motani ndi Mpingo Wathu?LERO TIKUFUNA TIONE KUTI KODI TIPEMBEDZE MOTANI NDI MPINGO WATHU?Tikudziwa chifukwa chimene mpingo ukuyenelera kukumana pamodzi. Koma ndi zinthu ziti zimene zingapangitse anthu kulephela kukumana ndi anzawo nthawi ya chipembedzo?Pali zifukwa zingapo zimene zingapelekedwe zolepheletsa anthu kukumana ndi anzawo nthawi ya chipembedzo. Ena amanena kuti iwo amaonetsela chikhulupiliro chawo mu njira zina. Ena amanena kuti sadapeze mpingo owasangalatsa. Ena amanena kuti sasangalatsidwa ndi ulaliki wa abusa awo. Ena amanena kuti samva kulandilidwa ku mpingo kwawo. Ena mukawafusa nthawi zonse amangoti ndi nadwala ndiye nkumadabwa kuti kodi abale muzingodwala pasabata pokhapokha?Ena...2021-07-0929 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chifukwa chiyani mpingo umakumana pamodzi?LERO TIKUFUNA TIONE KUTI KODI NDI CHIFUKWA CHIYANI MPINGO UMAKUMANA PAMODZI.Pali zinthu zambiri zimene titha kunena zokhudzana ndi chifukwa chimene mpingo umakumanila pamodzi – kupemphera, kukhala pa chiyanjano, kuphuzitsidwa, kupembedza Mulungu, ndi zina.Lero tikhazikika pa ndime imene imatiuza chifukwa chimodzi chimene chimapangitsa mpingo kuti uzikumana pamodzi komanso tiona chifukwa chimene kukumana kumeneku ndi ntchito yofunikila kwambiri pa mpingo.TIYENI TIWERENGE AHEBERI 10:19-25“Ndipo tsono abale, molimba mtima timalowa mʼMalo Opatulika kwambiri chifukwa cha magazi a Yesu. 20Iye anatitsekulira njira yatsopano ndi yamoyo kudutsa chinsalu chotchinga, chimene ndi thupi lake. 21Ndipo...2021-06-2226 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiUdindo wa Azimayi mu MpingoLERO TIKUFUNA TIONE ZA UDINDO WA AZIMAYI MU MPINGOGenesis 1:26-27; 2:19-251 Timothy 2:8-15Chiphuzitso cha mpingo ndicho chimene tikulondola.Mongokumbutsana tizindikile kunena kuti ulamuliro wathu pa china chilichonse chimene tifuna kuphuzila umachokela m’Baibulo. Ndi chifukwa chake pamene timayamba program imeneyi ya Chuma Mzikho Zadothi, tidayamba kuona kuti kodi Baibulo ndi chani. Cholinga chake chinali cha kuti tidzipatse poyambila kuti china chilichonse chokambidwa pa program imeneyi chichokele m’Mawu a Mulungu.POYAMBA TIYENI TIONE MTSUTSO UMENE UMAKHALAPO PA NKHANI YA UDINDO WA AMAYI MU MPINGO.Ayuda ena...2021-06-2228 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi amatsogolera mpingo ndi ndani?Khristu ndiye mutu wa mpingo. Akolose 1:18 akunena kuti: Iye ndiyenso mutu wa thupi, limene ndi mpingo. Iye ndiye chiyambi chake, woyamba kuuka kwa akufa, kuti Iyeyo akhale wopambana zonse.Nanga izi zikutanthauzanji pa zochitika za pa mpingo? Zikutanthauza kuti mpingo ukuyenela kumvera Mawu a Khristu pa china chilichonse chimene mpingo umachita. Pamapeto pa zonse, Khristu ndiye amene “amayendetsa” mpingo osati abusa anu kapena akuluampingo anu. Abusa ndi akuluampingo akuyenela kutsogolera mpingo momvera Mawu ake a Khristu basi. Mpingo ukuyenela kutsatila cholinga cha Khristu, osati zina.Ndiye funso lina nkumati, ngati Khristu ndi mutu wa mpingo, ndi...2021-06-0929 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi mpingo umagwila ntchito motani?1 Akorinto 12:12-26Thupi Limodzi Ziwalo Zambiri12Thupi ndi limodzi, ngakhale kuti lapangidwa ndi ziwalo zambiri. Ndipo ngakhale ziwalo zake zonse ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi. Momwemonso ndi mmene alili Khristu. 13Pakuti tonse tinabatizidwa ndi Mzimu mmodzi mʼthupi limodzi. Myuda kapena Mgriki, kapolo kapena mfulu tonse tinapatsidwa kuti timwe Mzimu mmodzi yemweyo. 14Tsopano thupi silinapangidwe ndi chiwalo chimodzi koma ndi ziwalo zambiri.15Ngati phazi litanena kuti, “Pakuti sindine dzanja, sindine chiwalo cha thupi.” Chifukwa chimenechi sichingachititse phazi kuti lisakhale chiwalo cha thupi. 16Ndipo ngati khutu litanena kuti, “Pakuti sindine diso, sindine chiwalo cha thupi.”...2021-05-3128 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chiyani chimene chimapangitsa mpingo kukhala opambana?Lero tikufuna tione chimene chimapangitsa mpingo kukhala opambana. Ndiye poyamba tiyeni tione kuti kodi ndi chiyani chimene chimapanga mpingo kukhala osiyana ndi mabungwe ena achikhristu?Poyankha funso limeneli ndiwelenge mutu 29 wa Chivomelezo cha ku Belgium chimene chidalembedwa m’chaka cha 1567 ndi Guido de Bres amene adali m’laliki m’mipingo ya chikonzedwe ku Netherlands ndipo adaphedwa chifukwa cha chikhulupiliro chake m’chaka chomwecho.Chimene chidachitika ndi chakuti, nthawi imeneyi mipingo yak u Netherland inali pa chizuzo choopsya ndi utsogoleri wa boma wa chiroma. Ndiye ngati gawo limodzi lolimbana ndi kuzuzidwa kwawoko, komanso kuonetsela kwa owazuzawo kuti mip...2021-05-3129 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi mpingo ndi chani?Sabata ino tikuyamba kuona zokhudzana ndi mpingoPalibe chinthu chopambana kuposa kukhala pa mpingo. Mpingo ngati banja la ana a Mulungu, limakhala ndi udindo waukulu pa wina ndi mnzake.Alipo anthu ena lero amene sazindikila bwinobwino udindo wa mpingo pa moyo wawo. Amaona ngati kulumikizana ndi Mulungu pawokha ndi bwino kusiyana ndi kukhazikika pa mpingo. Mwina kumayika patsogolo zinthu ngati mpira, kugona kapena maphuzilo pamwamba pa mpingo. Kuonjezela pamenepo, nthawi zina kumapezeka kuti timautumiki tina tikufuna kukhala pamwamba pa mpingo mpaka kupangila ma membala atchalitchi kumadzipeleka kwakukulu ku utumiki uja kusiyana ndi ku mpingo kwawo.2021-05-3126 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTiyambe motani kuwerenga Baibulo?Tsopano tafika gawo lathu lomaliza. Ndikhulupilira kuti pofika pano muli ndi chidziwitso chozama komanso kuvetsetsa kwabwino pa zimene Mawu a Mulungu ali. Mu njira ina, kuvetsetsa kwabwino kumeneku kwa Mawu a Mulungu kutha kutifoketsanso. Kutanthauza kuti, tavetsa bwino za kuzama kwa Baibulo komanso m’mene anthu ophuzila akangalika m’moyo wawo kulisanthula; pa chifukwa ichi, kuwerenga Baibulo itha kuoneka ntchito yovuta zedi. Lero tikufuna tione pamene tingayambile.Tiyambe ndi nkhani yapempheroNdiye ndineneletu kuti sititenga nthawi yaitali kukamba nkhani ya pemphero, chifukwa phuzilo lathu la 7 tidakamba kale zambiri zambiri. Tidaona kunena kuti tipemphere kuti tikhale ndi...2021-05-3129 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chifukwa chiyani tili ndi ma translation ambiri?Ndiye ndi chifukwa chiyani tili ndi ma translation ambiri?Monga ndinanena kale, Monga ndinanena kale, anthu ena amaganiza kunena kuti kupezeka kwa ma translation ambiri kumatsimikizila kuti Baibulo lili ndi zolakwika zambiri, koma tiyeni tione nkhani imeneyi mozama. Ndiyambe ndi kufusa funso ili, kodi Mose amawerenga translation yanji ya Baibulo? Yankho ake ndi lakuti, padalibe Baibulo la Mose. Timadziwa kuti Mose adalemba mabuku asanu oyambilira a Baibulo amene amatchedwanso Pentatuku, adalemba atatuluka ku Egypt ndipo pa gawo lalikulu la moyo wake adalibe mabuku asanu amenewa. Adali ndi timagawo, koma osati monga tili nalo lero lino. Imfa yake...2021-05-3128 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chifukwa chiyani nkovuta kuwerenga Baibulo?Pali zifukwa zambiri zimene zimapangitsa kuwerenga Baibulo kukhala chinthu chovuta, koma chifukwa chodziwikilatu – komanso chokhazikika – chimene chimapangitsa kuwerenga Baibulo kukhala chinthu chovuta ndi tchimo. Tikuyenela kuvomeleza kuti uchimo umatisokoneza.Ø Aefeso 2:1-3 akunena kuti: “Ndipo inu adakupatsani moyo, pokhala mudali akufa ndi zolakwa ndi zochimwa zanu; Zimene mudayendamo kale, monga mwa mayendedwe adziko lapansi lino, monga mwa mkulu wa ulamuliro wamlengalenga, wa mzimu wakuchita tsopano mwa ana akusamvera. Amene ife tonsenso tidagonera pakati pawo kale, mzilakolako za thupi lathu, ndi kuchita chifuniro cha thupi, ndi za maganizo, ndipo tidali ana a mkwiyo chibadwire, monganso wotsalawo.”Ø Ndime imeneyi ik...2021-05-3128 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo timawerenga motani? Gawo 3Lero tiyeni tiyambe ndi kuona mitundu ya Chipangano Chatsopano. Ndidatchula magawo anayi akuluakulu: Uthenga Wabwino, Mbiri, Makalata, komanso Mavumbulutso a Chimalizilo.Magawo amenewa titha kuwatambasula motere:Ø Uthenga Wabwino ndi mabuku anayi oyambilira a m’Chipangano Chakale. Mateyu, Marko, Luka komanso Yohane. Mabuku amenewa amatifotokozera zimene adaona za moyo, imfa, komanso kuuka kwa Yesu Khristu. Ndipo iwo akulemba izi monga nkhani.Ø Tikafika ku Mbiri: Buku la Machitidwe limafotokozela chiyambi cha mpingo wakale, kutsatira imfa ya Khristu. Luka ndiye amene adalemba buku la Machitidwe. Ndipo buku limeneli limatengedwa kuti ndi lotsatila Uthenga Wabwino wa Luka.2021-04-2125 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo timawerenga motani? Gawo 2Chinthu choyamba chimene tikufuna tikhazikikepo ndi nkhani ya dongosolo la magawidwe ake.Tidaona kale kuti Baibulo ndi nkhani imodzi imene yagawidwa mzipangano ziwiri.Ø Chipangano Chakale – chimene chili ndi magawo ake asanu akuluakulu ndipo magawo ake ndi awa: Mbiri, Chilamulo, Ndakatulo, Nzeru, komanso Aneneri (Akulu komanso Ang’ono).Ø Ndiye pali Chipangano Chatsopano – chimene chili ndi magawo ake anayi akuluakulu omwe ndi: Uthenga Wabwino, Mbiri, Makalata, komanso Mavumbulutso a Chimalizilo.Ø Tsopano chimene tikuyenela kuzindikila ndi chakuti: simungathe kuwerenga mabuku onse a m’Baibulo mofanana. Inde, taona kale kuti tikuyenela kufikila mabuku onse mwakupemphera – modzichepetsa...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo timawerenga motani?Ndiye tiyeni tifike pa funso lakuti: kodi Baibulo timawerenga motani? Litha kuoneka ngati funso lodabwitsa kwambiri popeza ambiri mwina timadziwa kuwerenga Baibulo. Koma chimene tikufuna tione ndi chakuti, Baibulo ndi losiyana ndi mabuku ena onse amene adalembedwa, ndi chifukwa chake akhristu akuyenela kufikila kuwerenga Malemba Opatulika mosiyanitsa ndi mabuku ena.Chinthu choyamba chimene tikufuna tichione ndi chakuti, tikuyenela tiwerenge Baibulo mwauzimu.Ahebri 4:12-13 akunena kuti: “Pakuti mawu a Mulungu ali a moyo, ndi wochitachita, ndi akuthwa koposa lupanga lakuthwa konse konse, napyoza kufikira kugawira moyo ndi mzimu, ndi zimfundo ndi mafuta a m’mafupa, nazindikiritsa zoli...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo limatiphuzitsa zotani: gawo 2Ndime imene tiyambe kuwerenga ndi Yakobo 2:14-26. “Chipindulo chake n’chiyani, abale anga, munthu akanena kuti ali nacho chikhulupiriro, koma alibe ntchito? Kodi chikhulupiriro chotere chikhoza kumpulumutsa? Ngati mchimwene kapena mlongo wavala movetsa chisoni, nasowekela chakudya cha tsiku lake, ndipo wina wa inu nanena nawo, ‘Mukani ndi mtendere, mukafunditsidwe ndi kukhuta,’ osawapatsa iwo zosowa za ku thupi; kupindula kwake n’chiyani? Momwemonso chikhulupiliro pachokha, chikapanda kukhala nazo ntchito, chili chakufa.Koma wina atha kunena, ‘Iwe uli nacho chikhulupiliro, ndipo ine ndiri nazo ntchito.” Tandionetsa ine chikhulupiliro chako chopanda ntchito zako, ndipo ine ndidzakuwonetsa iwe chikhulupiliro changa kudzera m’nchito zanga...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo limatiphuzitsa zotani: gawo 1Tiyambe kuona za chipulumutso. 2 Timoteo 3:12-15. “Zoonadi, onse akufuna kukhala moyo wachiyero mwa Khristu Yesu, adzazuzidwa pamene anthu woyipa ndi wonyenga, adzayipa chiyipile, kunama ndi kunamizidwa. Koma iwe, ukhalebe mu zinthu zimene waziphunzira, ndi kuzikhulupilira motsimikizika, podziwa amene adakuphunzitsa ndi m’mene kuyambira umwana wako wadziwa malembo wopatulika, wokhoza kukupatsa nzeru kufikira chipulumutso, kudzera mwa chikhulupiriro cha mwa Khristu Yesu.”Chinthu chimodzi chofunikila kwambiri chimene tikuyenela kudziwa ndi chakuti Malemba Opatulika ali ndi kuthekela “kukupatsa nzeru kufikila chipulumutso kudzera m’chikhulupiliro cha mwa Yesu Khristu."2021-03-2537 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo Limakamba Zotani?Tiyeni tiwerenge Mateyu 22:34-40“Koma pamene Afarisi adamva kuti Iye adasowetsa chokamba Asaduki, adasokhana pamodzi. Ndipo m’modzi wa iwo, mphunzitsi wa chilamulo, adamfunsa Iye funso kuti amuyese Iye. ‘Mphunzitsi, lamulo lalikulu ndi liti la m’chilamulo?’ Ndipo Iye adati kwa iye, ‘Uzikonda Ambuye Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse ndi maganizo ako onse. Ili ndilo lamulo lalikulu ndi loyamba. Ndipo lachiwiri lofanana nalo ndi ili, Uzikonda mzako monga iwe mwini. Pa malamulo awiriwa pamatsamila chilamulo chonse ndi aneneri.’”Pa ndime imeneyi, Yesu akunena kuti chilamulo chonse komanso zolemba zonse za aneneri zifupiki...2021-03-1726 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiBaibulo lidalembedwa chifukwa chiyani?Ndiye ndi mawu amene akupezeka pa Genesis 1:1 china chilichonse m’moyo chikupatsidwa maonekedwe ake, cholinga chake komanso tanthauzo lake. Ndi chinthu chofunikila komanso kudzichepetsa kuzindikila kuti nkhani ya Baibulo siyidayambe ndi ife. Imayamba ndi Mulungu. Ndi chinthu chofunikila kwambiri kuzindikila kuti pamene nkhani ya masamba a Baibulo ikutambasulidwa ndi nkhani ya Mulungu. Iye wayima pakatipati pa zochitika zonse. Iye ali ndi magawo ofunikila. China chilichonse chikudalira Iye. Nkhaniyo ikuyenda monga mwa chifunilo chake komanso dongosolo lake. Zonse ndi za Iye, zochokela kwa Iye, kudzera mwa Iye, komanso zokhudzana ndi Iye.Ndiye pamenepa titha kupezapo yankho pa funso la...2021-03-0732 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiBaibulo ndi chani?Tikaona pa vesi 15 ya 2 Timoteo chapter 3 Paulo akutiuza kuti Malemba Opatulika ali ndi kuthekela kutiunikila za chipulumutso kudzera mwa chikhulupiliro cha mwa Yesu Khristu. Ichi ndi chilungamo chochokela m’Baibulo chimene tikhazikikapo tsiku la lero. Baibulo ndi buku lodabwitsa limene lili ndi mphamvu zopulumutsa anthu osakhulupilira chifukwa choti Baibulo limalozela anthu kwa Yesu Khristu. Tikawelenganso Aheberi 4:12 tiona kuti Baibulo lili ndi moyo wodabwitsa.2021-03-0527 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTanthauzo la BaibuloKuwerenga Baibulo ndi kofunikila kwambiri. Tikaphuzitsa mtundu wa akhristu amene akudziwa kuphuzila, kukhala komanso kukonda Mau a Mulungu, tidzawakozekeletsa kukumana ndi china chilichose chobwela m’dziko.Tikakamba za Baibulo tikutanthauza za mabuku 66 ogawidwa mu zipangano ziwiri. Chipangano chakale mabuku 39 komanso chatsopano mabuku 27.Tikawelenga Baibulo timaphuzila zambiri za m’mene munthu alili komanso tanthauzo la moyo. Limatidziwitsa za Mulungu amene anatilenga komanso amene ali gwelo la dziko lonse. Mulungu amadzivumbulutsa yekha kwa ife kudzera m’Baibulo amene afunanso kuyanjana nafe.2021-03-0223 min