Look for any podcast host, guest or anyone
Showing episodes and shows of

Zonse Live

Shows

Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaTisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaChitonthozo Cha Mulungu Mzinthu Zonse Pa Utumiki Wa Kristu2025-04-1827 minTisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaTisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaChitonthozo Cha Mulungu Mu Nyengo Zonse Za Utumiki Wa Kristu2025-04-1727 minTisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaTisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewaChikondi Ndiyo Mphamvu Ya Mphatso Zonse2025-02-2726 minSpill The Tearal: A JRPG PodcastSpill The Tearal: A JRPG PodcastEpisode 40: Ranking Every Zenless Zonse Zero Character + JRPG Releases This WeekWelcome to Episode 40 of Spill the Tearal: A JRPG Podcast! This week I rank every Zenless Zone Zero character, speak about how I've been playing Zenless Zone Zero and Wuthering Waves, and discuss the JRPGs that released this week! Enjoy!2024-11-1448 minThis is the Bible BardThis is the Bible BardCicē'ōẏā_BB 04_Mulungu Amadziwa ChilichonseM’phunziro limeneli Baibulo limaphunzitsa kuti Mulungu amadziwa zonse. (BB-04)2024-07-2212 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiUmunthu wa Yesu KhristuPACHIYAMBI panali Mawu, ndipo Mawu adali ndi Mulungu, ndipo Mawu adali Mulungu. Awa adali pachiyambi ndi Mulungu. Zinthu zonse zidalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikadalengedwa kanthu kena kali konse kolengedwa. Mwa Iye mudali moyo; ndi moyowu udali kuwunika kwa anthu. Ndipo kuwunikaku kudawala mumdima; ndi mdimawu sudakuzindikira. Kudali munthu, wotumidwa ndi Mulungu, dzina lake ndiye Yohane. Iyeyu adadza mwa umboni, kudzachita umboni za kuwunikaku, kuti anthu onse kudzera mwa iye akakhulupirire. Iye sindiye kuwunikaku, koma adatumidwa kukachita umboni wa kuwunikaku. Uku ndiko kuwunika kwenikweni kumene kuwunikira anthu onse akulowa m’dziko lapansi. Adali m’dziko lapansi, ndipo dziko lapa...2022-05-2428 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 6Usaphe.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2425 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 10Usasirire.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 8Usabe.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miya...2022-05-2426 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 7Usachite chigololo.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado m...2022-05-2422 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo 9Usapereke umboni omunamizila mzako.EKSODO 20Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi ch...2022-05-2424 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKugwa kwa MunthuKuchimwa kwa Munthu1Ndipo njoka inali yochenjera kuposa nyama yakuthengo iliyonse imene Yehova Mulungu anapanga. Njokayo inati kwa mkaziyo, “Kodi Mulungu ananenadi kuti, ‘Inu musadye zipatso za mtengo uliwonse mʼmundamu?’ ”2Mkaziyo anati kwa njokayo, “Tikhoza kudya zipatso za mʼmitengo ya mʼmundawu, 3koma Mulungu anati, ‘Musadye zipatso za mu mtengo umene uli pakati pa munda, ndipo musadzawukhudze kuti mungadzafe.’ ”4“Ndithudi simudzafa,” inatero njokayo kwa mkaziyo. 5“Pakuti Mulungu akudziwa kuti tsiku limene mudzadye zipatso za mu mtengowo, maso anu adzatsekuka, ndipo mudzakhala ngati Mulungu, wodziwa zabwino ndi zoyipa.”6Pamene mkaziyo anaona kuti mtengowo unali wabw...2022-05-2427 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKufunikila kwa Imfa ya Ambuye YesuKoma atafika Khristu, Mkulu wansembe wa zabwino ziri mkudza, mwa chihema chachikulu ndi changwiro choposa, chosamangika ndi manja, ndiko kunena kuti, chosati cha chilengedwe ichi; Kosati mwa mwazi wa mbuzi ndi ana ang’ombe, koma mwa mwazi wa Iye yekha, adalowa kamodzi kumalo wopatulika, atalandirapo chiwombolo chosatha chifukwa cha ife. Pakuti ngati mwazi wa mbuzi ndi ng’ombe zamphongo, ndi makala ang’ombe yamthandi wowazawaza pa iwo wodetsedwa, upatutsa kufikira chiyeretso cha thupi: Koposa kotani nanga mwazi wa Khristu amene adadzipereka yekha wopanda chilema kwa Mulungu mwa Mzimu wosatha, udzayeretsa chikumbumtima chanu kuchisiyanitsa ndi ntchito zakufa, kukatumikira Mulungu wamoyo? Ndipo...2022-05-2426 minSomething RadioSomething RadioCan we be good Wedding Mc's ? | Has Data Fallen ? | Jeen Yuh's | Mental Health | SR EP 13We have been honored to host a couple of shows around the country, we are thinking of expanding and Hosting wedding soon. Would you invite us to host your Special day ? Malawi's two cellular internet service providers announced reduced data Plans, Only to learn that they are three months promotion, Has Data really fallen ? We Talk about "Jeen Yuh's" A Kanye West Documentary that has given us so much light on how the artist has evolved Musically. We discuss the mental Health and how best we can do better. Enjoy these plus more topics we discuss.   2022-03-1141 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo LachisanuMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0824 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiLamulo LachinayiMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0825 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMalamulo Khumi Gawo 2Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0825 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiMalamulo Khumi Gawo 1Malamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0827 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiUdindo wa MunthuMalamulo Khumi1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati:2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo.3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.”4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko. 5Usazigwadire kapena kuzipembedza, pakuti Ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wansanje, wolanga ana chifukwa cha tchimo la makolo awo mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo amene amadana nane. 6Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.2022-03-0824 minSomething RadioSomething Radio"I wanted to get peoples reactions" - Gwamba Responds to twitter.After the Rapper announced his upcoming album by publishing just the artwork, twitter Malawi went on to critic it. The Rapper now gives his full insight on what he wanted to achieve by releasing it like that. David Page and Tyfrequency engage him more by asking him by playing a game called either all ( made up on the spot)2022-01-111h 08Chuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiTanthauzo la PempheroAroma 8:26-2826Momwemonso, Mzimu amatithandiza ife mʼkufowoka kwathu. Ife sitidziwa momwe tiyenera kupempherera koma Mzimu mwini amatipempherera mobuwula ndi mawu osafotokozedwa. 27Koma Iye amene amasanthula mitima yathu amadziwa maganizo a Mzimu, chifukwa Mzimu amapempherera oyera mtima molingana ndi chifuniro cha Mulungu. 28Ndipo ife tikudziwa kuti zinthu zonse zimathandizana kuwachitira ubwino amene amakonda Mulungu, amene anayitanidwa monga mwa cholinga chake.2021-09-1827 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiChikhalidwe Komanso Tanthauzo la MgoneroChikhalidwe komanso Tanthauzo la Mgonero wa AmbuyeTikumbukile nthawi imene timakamba za masakalamenti pamene tidanena kuti alipo awiri: ubatizo komanso mgonero wa Ambuye.Masakalamenti amenewa adakhazikitsidwa ndi cholinga choti aonetsele poyera chikhulupiliro chathu cha uthenga wabwino. Pamene tikondwelera mu mgonero wa Ambuye komanso kutenga mbali pa ubatizo, zonsezi zimatipatsa mwayi oti tionetsele chikhulupiliro chathu poyera.Anthu atatipeza natifusa kuti kodi ndi chifukwa chiyani mukuchita izi. Yankho lake ndi lakuti, chifukwa cha chimene Yesu Khristu ali komanso zimene adachita. St. Augustine pokamba za masakalamenti adanena kuti: “zizindikilo zakunja komanso zooneka ndi maso za chisomo ch...2021-07-0927 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Tipembedze Motani ndi Mpingo Wathu?LERO TIKUFUNA TIONE KUTI KODI TIPEMBEDZE MOTANI NDI MPINGO WATHU?Tikudziwa chifukwa chimene mpingo ukuyenelera kukumana pamodzi. Koma ndi zinthu ziti zimene zingapangitse anthu kulephela kukumana ndi anzawo nthawi ya chipembedzo?Pali zifukwa zingapo zimene zingapelekedwe zolepheletsa anthu kukumana ndi anzawo nthawi ya chipembedzo. Ena amanena kuti iwo amaonetsela chikhulupiliro chawo mu njira zina. Ena amanena kuti sadapeze mpingo owasangalatsa. Ena amanena kuti sasangalatsidwa ndi ulaliki wa abusa awo. Ena amanena kuti samva kulandilidwa ku mpingo kwawo. Ena mukawafusa nthawi zonse amangoti ndi nadwala ndiye nkumadabwa kuti kodi abale muzingodwala pasabata pokhapokha?Ena...2021-07-0929 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi amatsogolera mpingo ndi ndani?Khristu ndiye mutu wa mpingo. Akolose 1:18 akunena kuti: Iye ndiyenso mutu wa thupi, limene ndi mpingo. Iye ndiye chiyambi chake, woyamba kuuka kwa akufa, kuti Iyeyo akhale wopambana zonse.Nanga izi zikutanthauzanji pa zochitika za pa mpingo? Zikutanthauza kuti mpingo ukuyenela kumvera Mawu a Khristu pa china chilichonse chimene mpingo umachita. Pamapeto pa zonse, Khristu ndiye amene “amayendetsa” mpingo osati abusa anu kapena akuluampingo anu. Abusa ndi akuluampingo akuyenela kutsogolera mpingo momvera Mawu ake a Khristu basi. Mpingo ukuyenela kutsatila cholinga cha Khristu, osati zina.Ndiye funso lina nkumati, ngati Khristu ndi mutu wa mpingo, ndi...2021-06-0929 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi mpingo umagwila ntchito motani?1 Akorinto 12:12-26Thupi Limodzi Ziwalo Zambiri12Thupi ndi limodzi, ngakhale kuti lapangidwa ndi ziwalo zambiri. Ndipo ngakhale ziwalo zake zonse ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi. Momwemonso ndi mmene alili Khristu. 13Pakuti tonse tinabatizidwa ndi Mzimu mmodzi mʼthupi limodzi. Myuda kapena Mgriki, kapolo kapena mfulu tonse tinapatsidwa kuti timwe Mzimu mmodzi yemweyo. 14Tsopano thupi silinapangidwe ndi chiwalo chimodzi koma ndi ziwalo zambiri.15Ngati phazi litanena kuti, “Pakuti sindine dzanja, sindine chiwalo cha thupi.” Chifukwa chimenechi sichingachititse phazi kuti lisakhale chiwalo cha thupi. 16Ndipo ngati khutu litanena kuti, “Pakuti sindine diso, sindine chiwalo cha thupi.”...2021-05-3128 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chiyani chimene chimapangitsa mpingo kukhala opambana?Lero tikufuna tione chimene chimapangitsa mpingo kukhala opambana. Ndiye poyamba tiyeni tione kuti kodi ndi chiyani chimene chimapanga mpingo kukhala osiyana ndi mabungwe ena achikhristu?Poyankha funso limeneli ndiwelenge mutu 29 wa Chivomelezo cha ku Belgium chimene chidalembedwa m’chaka cha 1567 ndi Guido de Bres amene adali m’laliki m’mipingo ya chikonzedwe ku Netherlands ndipo adaphedwa chifukwa cha chikhulupiliro chake m’chaka chomwecho.Chimene chidachitika ndi chakuti, nthawi imeneyi mipingo yak u Netherland inali pa chizuzo choopsya ndi utsogoleri wa boma wa chiroma. Ndiye ngati gawo limodzi lolimbana ndi kuzuzidwa kwawoko, komanso kuonetsela kwa owazuzawo kuti mip...2021-05-3129 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiNdi chifukwa chiyani nkovuta kuwerenga Baibulo?Pali zifukwa zambiri zimene zimapangitsa kuwerenga Baibulo kukhala chinthu chovuta, koma chifukwa chodziwikilatu – komanso chokhazikika – chimene chimapangitsa kuwerenga Baibulo kukhala chinthu chovuta ndi tchimo. Tikuyenela kuvomeleza kuti uchimo umatisokoneza.Ø Aefeso 2:1-3 akunena kuti: “Ndipo inu adakupatsani moyo, pokhala mudali akufa ndi zolakwa ndi zochimwa zanu; Zimene mudayendamo kale, monga mwa mayendedwe adziko lapansi lino, monga mwa mkulu wa ulamuliro wamlengalenga, wa mzimu wakuchita tsopano mwa ana akusamvera. Amene ife tonsenso tidagonera pakati pawo kale, mzilakolako za thupi lathu, ndi kuchita chifuniro cha thupi, ndi za maganizo, ndipo tidali ana a mkwiyo chibadwire, monganso wotsalawo.”Ø Ndime imeneyi ik...2021-05-3128 minNews in ChinyanjaNews in ChinyanjaZambia political parties choose female candidatesCHINYANJA: Pafupi fupi zipani zonse mdziko la Zambia zasankha amayi kukhala achiwiri kwa atsogoleri pomwe azapikisane pa masankho a pa 12 August 2021. ENGLISH: Almost all political parties have chosen women as running mates for their leaders as they prepare for the August 12 elections.2021-05-2105 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo timawerenga motani? Gawo 2Chinthu choyamba chimene tikufuna tikhazikikepo ndi nkhani ya dongosolo la magawidwe ake.Tidaona kale kuti Baibulo ndi nkhani imodzi imene yagawidwa mzipangano ziwiri.Ø Chipangano Chakale – chimene chili ndi magawo ake asanu akuluakulu ndipo magawo ake ndi awa: Mbiri, Chilamulo, Ndakatulo, Nzeru, komanso Aneneri (Akulu komanso Ang’ono).Ø Ndiye pali Chipangano Chatsopano – chimene chili ndi magawo ake anayi akuluakulu omwe ndi: Uthenga Wabwino, Mbiri, Makalata, komanso Mavumbulutso a Chimalizilo.Ø Tsopano chimene tikuyenela kuzindikila ndi chakuti: simungathe kuwerenga mabuku onse a m’Baibulo mofanana. Inde, taona kale kuti tikuyenela kufikila mabuku onse mwakupemphera – modzichepetsa...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo timawerenga motani?Ndiye tiyeni tifike pa funso lakuti: kodi Baibulo timawerenga motani? Litha kuoneka ngati funso lodabwitsa kwambiri popeza ambiri mwina timadziwa kuwerenga Baibulo. Koma chimene tikufuna tione ndi chakuti, Baibulo ndi losiyana ndi mabuku ena onse amene adalembedwa, ndi chifukwa chake akhristu akuyenela kufikila kuwerenga Malemba Opatulika mosiyanitsa ndi mabuku ena.Chinthu choyamba chimene tikufuna tichione ndi chakuti, tikuyenela tiwerenge Baibulo mwauzimu.Ahebri 4:12-13 akunena kuti: “Pakuti mawu a Mulungu ali a moyo, ndi wochitachita, ndi akuthwa koposa lupanga lakuthwa konse konse, napyoza kufikira kugawira moyo ndi mzimu, ndi zimfundo ndi mafuta a m’mafupa, nazindikiritsa zoli...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo limatiphuzitsa zotani: gawo 2Ndime imene tiyambe kuwerenga ndi Yakobo 2:14-26. “Chipindulo chake n’chiyani, abale anga, munthu akanena kuti ali nacho chikhulupiriro, koma alibe ntchito? Kodi chikhulupiriro chotere chikhoza kumpulumutsa? Ngati mchimwene kapena mlongo wavala movetsa chisoni, nasowekela chakudya cha tsiku lake, ndipo wina wa inu nanena nawo, ‘Mukani ndi mtendere, mukafunditsidwe ndi kukhuta,’ osawapatsa iwo zosowa za ku thupi; kupindula kwake n’chiyani? Momwemonso chikhulupiliro pachokha, chikapanda kukhala nazo ntchito, chili chakufa.Koma wina atha kunena, ‘Iwe uli nacho chikhulupiliro, ndipo ine ndiri nazo ntchito.” Tandionetsa ine chikhulupiliro chako chopanda ntchito zako, ndipo ine ndidzakuwonetsa iwe chikhulupiliro changa kudzera m’nchito zanga...2021-04-0931 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiKodi Baibulo Limakamba Zotani?Tiyeni tiwerenge Mateyu 22:34-40“Koma pamene Afarisi adamva kuti Iye adasowetsa chokamba Asaduki, adasokhana pamodzi. Ndipo m’modzi wa iwo, mphunzitsi wa chilamulo, adamfunsa Iye funso kuti amuyese Iye. ‘Mphunzitsi, lamulo lalikulu ndi liti la m’chilamulo?’ Ndipo Iye adati kwa iye, ‘Uzikonda Ambuye Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse ndi maganizo ako onse. Ili ndilo lamulo lalikulu ndi loyamba. Ndipo lachiwiri lofanana nalo ndi ili, Uzikonda mzako monga iwe mwini. Pa malamulo awiriwa pamatsamila chilamulo chonse ndi aneneri.’”Pa ndime imeneyi, Yesu akunena kuti chilamulo chonse komanso zolemba zonse za aneneri zifupiki...2021-03-1726 minChuma mzikho zadothiChuma mzikho zadothiBaibulo lidalembedwa chifukwa chiyani?Ndiye ndi mawu amene akupezeka pa Genesis 1:1 china chilichonse m’moyo chikupatsidwa maonekedwe ake, cholinga chake komanso tanthauzo lake. Ndi chinthu chofunikila komanso kudzichepetsa kuzindikila kuti nkhani ya Baibulo siyidayambe ndi ife. Imayamba ndi Mulungu. Ndi chinthu chofunikila kwambiri kuzindikila kuti pamene nkhani ya masamba a Baibulo ikutambasulidwa ndi nkhani ya Mulungu. Iye wayima pakatipati pa zochitika zonse. Iye ali ndi magawo ofunikila. China chilichonse chikudalira Iye. Nkhaniyo ikuyenda monga mwa chifunilo chake komanso dongosolo lake. Zonse ndi za Iye, zochokela kwa Iye, kudzera mwa Iye, komanso zokhudzana ndi Iye.Ndiye pamenepa titha kupezapo yankho pa funso la...2021-03-0732 minSomething RadioSomething RadioThoughts On ThirdEye's Career, AKA & Riky Rick Apologies, Hayze Engola KNQR ShopIn today's episode, we talk about the thoughts a Facebook run entertainment page have on Malawian rapper Third Eye's career. South African rappers AKA and Riky Rick apologized to Sizwe Dhlomo about their online banter and Hayze Engola just opened the first KNQR shop in Blantyre Malawi. 2020-06-0549 minSomething RadioSomething RadioDrama Industry | AKA VS Reebok & Sizwe Dhlomo, Malawi's Frist OnlyFans Account, Malawi Hip Hop AwardsIn today's episode we discuss all things new music with Future and Kehlani's new album. We also discuss the AKA Reebok drama that seems to have landed him into an online back and forth with Sizwe Dhlomo. Rapper Gwamba announced the Malawi Hip Hop awards and did Malawi just get its first Only Fans Account ?? 2020-05-2247 minChiphunzitso Choona | Sound Doctrine from Gospel Life Global MissionsChiphunzitso Choona | Sound Doctrine from Gospel Life Global MissionsSonkhani Pamodzi kuti Mupembeze | Gather for WorshipMachitidwe 2:42; Ahebri 10:24–25. Timasokhana pamodzi kuti tipembeze ndi cholinga choti tithandizone wina ndi nzake kukula musinkhu mwa Khristu. Tikuyenera kukhala ndi chikhalidwe chopembera ndi mpingo umodzi nthawi zonse. Acts 2:42; Hebrews 10:24–25. We gather to worship to help one another grow to maturity in Christ. We must make worship with our church a habit. Preacher: Dr. Joshua Hutchens Class: Kukhala Wophunzira: Kukhala Moyo Wosinthika ndi Uthenga Wabwino | Discipleship: Living the Gospel Translator: Isaac Dzimbiri2020-05-1930 minSomething RadioSomething RadioGwamba & Fredo Spending Big on Eli Njuchi & Phyzix Projects, Liwu New SingleGwamba and Fredokiss spent big on both Eli Njuchi and Phyzix's albums. Phyzix was able to sell his for millions. Does this make him a legend?   Also would you buy a 1k project at 50k with your “hard earned money?”2020-04-3028 minSomething RadioSomething RadioBlazered Up Part1In this episode, we discuss the difference between a producer and a beat maker. Malawian rapper Phyzix also announced that he would be executive producing the new Daredevils project. We are joined by a special guest, Artist and Entrepreneur Mac Ndalama2020-04-3028 minSomething RadioSomething RadioSelling The StruggleIn this Episode, The boys talk about Malawian rapper Fredokiss supposedly selling the struggle as he explains it to Wikise. They debate the famous iPhone vs Android argument and they reflect on the ongoing Dont Rush challenge as Malawians held their own. Also, new artist on the block Praise Umali finally released his latest single #Proud.2020-04-3039 minSomething RadioSomething RadioMoney For Airplay - Something Radio Ep3In today's episode, we have our first guest, TV/Radio and Event host Cynthia Zonde Zulu. They discuss the Malawi Zambia issue, Page's passion for Facebook, Ben Wandawanda's new upcoming fashion brand, Eli Njuchi's upcoming EP and Nasty C's new Def Jam deal.  2020-04-0345 minSomething RadioSomething RadioMalawian artists & Sponsorship Deals, Onesimus on BBC, Cassper vs AKA Boxing MatchIn This weeks episode, the boys discuss the different sponsorship deals Malawian artists get themselves in, taking a special focus on Hayze Engola's new Sports kit deal with soccer team Hungover United, through his KNQR brand.   Malawian Gospel artist Onesimus was hosted on BBC world and uhhmmm, a lot happened in that video. https://twitter.com/bbcworldservice/s...  Finally Cassper Nyovest and AKA are still at each others necks. Should they take it out in a boxing ring ?2020-03-2738 minSomething RadioSomething RadioNamadingo Vs Lulu, The Rona & Jamz Supanova Malawi tourIn our first episode, we discuss the Legendary talk between Patience Namadingo and Lulu. We discuss the effects The Rona has had on arts and entertainment in the world and we take a look back at BBC's dj Jamz Supanova's recent tour to Malawi. 2020-03-2734 minNews in ChinyanjaNews in ChinyanjaChnyanja News-Zochitika Mu AfricaMu programu yathu ya lero: 1. Aphungu a Nigeria akupnga malamulo okhudza aphunzitsi amene amanyengerera atsikana apa sukulu kugona nao 2. Anthu wobwera 20,000 anali mu ndende za South Africa kumapeto kwa mwezi wa June caka cino 3. Mapepa woponyera voti ndi katudu wina aperekedwa ku zigao zonse za Mozambique. Ndipo tilinso ndi nkhani zina zambiri. Stella Longwe ndi Madalitso Phiri akubweretserani programuyi.2019-10-1000 minWoza - This is AfricaWoza - This is AfricaChabwera Banda presents The M - Dub - Files (Malawian HipHop Mix 2012)A mix by Chabwera Banda (Woza - This is Africa) from 2012 representing some big Malawian rap tunes from LL to BT-City. M-Dub Woza Playlist Phyzix – Malawi HipHop BarryUno feat. Young Kay & Third Eye – All Red everything Mkotama – It’s so cold Inyct – Oh lalala Mphomusowa feat. Dare Devilz – Stop and stare Sonye feat. Inyct & Third Eye – Fight the System Inyct - Now Inyct – Keep pushing Dominant One – Need you Clau-D feat. Renegade - chaka China Phyzix – Mayi anga Mafuso – Malawiz Favourite People BarryUno feat. Wizdom & Khama – Umodzi BarryUno feat. Maskal – Zonse uiwale Dare Devilz feat. JB & Fredokiss - Ndimakonda akazi A.I. feat. Tay Grin & Yesa...2015-06-101h 13